Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+

  • 2 Samueli 11:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako Davide anatuma nthumwi kuti akamutenge.+ Choncho mkaziyo anabweradi kwa Davide+ ndipo Davide anagona naye+ pa nthawi imene mkaziyo anali kudziyeretsa ku chodetsa chake.+ Zitatero mkaziyo anabwerera kunyumba yake.

  • Yeremiya 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iwo akhala ngati mahatchi amphongo achilakolako champhamvu chofuna kukwera, okhala ndi mavalo amphamvu. Aliyense amamemesa* mkazi wa mnzake.+

  • Ezekieli 22:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu wachita zinthu zonyansa ndi mkazi wa mnzake,+ ndipo munthu wachita khalidwe lotayirira mwa kugona ndi mkazi wa mwana wake.+ Munthu wagona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena