Ekisodo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Usachite chigololo.+ Levitiko 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Usagone ndi mkazi wa mnzako* n’kukhala wodetsedwa.+ Levitiko 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu wochita chigololo ndi mkazi wa munthu wina, wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake.+ Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo aziphedwa ndithu.+ Deuteronomo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Mwamuna akapezeka akugona ndi mkazi wa mwiniwake,+ mwamuna ndi mkaziyo, onsewo azifera pamodzi. Mwamuna wogona ndi mkaziyo ndiponso mkaziyo azifera pamodzi.+ Motero uzichotsa oipawo mu Isiraeli.+ Miyambo 6:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense wochita chigololo ndi mkazi alibe nzeru mumtima mwake.+ Amene amachita zimenezi amawononga moyo wake.+ Aheberi 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+ Yakobo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+
10 “‘Munthu wochita chigololo ndi mkazi wa munthu wina, wachita chigololo ndi mkazi wa mnzake.+ Mwamuna ndi mkazi amene achita chigololowo aziphedwa ndithu.+
22 “Mwamuna akapezeka akugona ndi mkazi wa mwiniwake,+ mwamuna ndi mkaziyo, onsewo azifera pamodzi. Mwamuna wogona ndi mkaziyo ndiponso mkaziyo azifera pamodzi.+ Motero uzichotsa oipawo mu Isiraeli.+
32 Aliyense wochita chigololo ndi mkazi alibe nzeru mumtima mwake.+ Amene amachita zimenezi amawononga moyo wake.+
4 Ukwati ukhale wolemekezeka kwa onse, ndipo pogona pa anthu okwatirana pakhale posaipitsidwa,+ pakuti Mulungu adzaweruza adama ndi achigololo.+
15 Ndiye chilakolako chikatenga pakati, chimabala tchimo.+ Nalonso tchimo likakwaniritsidwa, limabweretsa imfa.+