Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pambuyo pake Mulungu anafikira Abimeleki usiku m’maloto n’kumuuza kuti: “Ufatu iwe chifukwa cha mkazi amene watengayu,+ pakuti ndi mkazi wa mwini.”+

  • Ekisodo 21:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ngati anabwera ali yekha, adzachokanso ali yekha. Ngati ali ndi mkazi, mkazi wakeyo adzapita naye.

  • Yesaya 62:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti monga momwe mnyamata amatengera namwali kuti akhale mkazi wake, ana ako aamuna adzakutenga kuti ukhale mkazi wawo.+ Monga momwe mkwati amakhalira wachimwemwe chifukwa cha mkwatibwi,+ Mulungu wako adzakhala ndi chimwemwe chifukwa cha iwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena