Yesaya 65:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzasangalala ndi Yerusalemu ndipo ndidzakondwera ndi anthu anga.+ Mwa iye simudzamvekanso kulira kokweza mawu kapena kulira kwachisoni.”+ Yeremiya 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndidzakondwera nawo ndi kuwachitira zabwino.+ Ndidzawabzala m’dziko lino+ mokhulupirika ndi mtima wanga wonse komanso ndi moyo wanga wonse.’”
19 Ndidzasangalala ndi Yerusalemu ndipo ndidzakondwera ndi anthu anga.+ Mwa iye simudzamvekanso kulira kokweza mawu kapena kulira kwachisoni.”+
41 Ndidzakondwera nawo ndi kuwachitira zabwino.+ Ndidzawabzala m’dziko lino+ mokhulupirika ndi mtima wanga wonse komanso ndi moyo wanga wonse.’”