Levitiko 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Usavule mpongozi wako wamkazi,+ chifukwa ndi mkazi wa mwana wako. Usam’vule. Levitiko 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwamuna akagona ndi mpongozi wake wamkazi, onse awiri aziphedwa ndithu.+ Iwo achita chinthu chosemphana ndi chibadwa. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.+ Ezekieli 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 (koma bamboyo sanachitepo chilichonse mwa zinthu zimenezi), ngati mwanayo amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano m’mapiri+ ndipo amaipitsa mkazi wa mnzake,+
12 Mwamuna akagona ndi mpongozi wake wamkazi, onse awiri aziphedwa ndithu.+ Iwo achita chinthu chosemphana ndi chibadwa. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.+
11 (koma bamboyo sanachitepo chilichonse mwa zinthu zimenezi), ngati mwanayo amadya chakudya choperekedwa nsembe kwa mafano m’mapiri+ ndipo amaipitsa mkazi wa mnzake,+