12 Mwamuna akagona ndi mpongozi wake wamkazi, onse awiri aziphedwa ndithu.+ Iwo achita chinthu chosemphana ndi chibadwa. Mlandu wa magazi awo ukhale wa iwo eni.+
11 Munthu wachita zinthu zonyansa ndi mkazi wa mnzake,+ ndipo munthu wachita khalidwe lotayirira mwa kugona ndi mkazi wa mwana wake.+ Munthu wagona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake.+