Levitiko 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Usavule mpongozi wako wamkazi,+ chifukwa ndi mkazi wa mwana wako. Usam’vule.