1 Samueli 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa. Yobu 33:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Adzaimbira anthu n’kunena kuti,‘Ndachimwa,+ ndakhotetsa zimene zinali zowongoka,Ndipo sindinayenere kuchita zimenezi. Miyambo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kulungama kwa anthu owongoka mtima n’kumene kudzawapulumutse,+ koma anthu ochita zinthu mwachinyengo adzagwidwa ndi zolakalaka zawo.+
17 Iye anapitiriza kuuza Davide kuti: “Ndiwe wolungama kwambiri kuposa ine,+ pakuti iwe wandichitira zabwino,+ koma ine ndakuchitira zoipa.
27 Adzaimbira anthu n’kunena kuti,‘Ndachimwa,+ ndakhotetsa zimene zinali zowongoka,Ndipo sindinayenere kuchita zimenezi.
6 Kulungama kwa anthu owongoka mtima n’kumene kudzawapulumutse,+ koma anthu ochita zinthu mwachinyengo adzagwidwa ndi zolakalaka zawo.+