Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 7:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mavuto ake adzabwerera pamutu pake,+

      Ndipo chiwawa chake chidzatsikira paliwombo pake.+

  • Miyambo 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+

  • Mlaliki 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Chimene chimamvetsa chisoni pa zinthu zonse zimene zimachitika padziko lapansi pano n’chakuti, popeza mapeto a anthu onse ndi amodzi,+ mtima wa ana a anthu ndi wodzazanso ndi zoipa.+ Mumtima mwawo mumakhala misala+ pa nthawi imene ali ndi moyo ndipo pamapeto pake, iwo amapita kwa akufa.+

  • Mlaliki 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Amene akukumba dzenje adzagweramo,+ ndipo amene akugumula mpanda wamiyala njoka idzamuluma.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena