Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Mwamuna akatenga mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake, n’kugona naye, chimenecho ndi chinthu chochititsa manyazi.+ Chotero onse awiri aziphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu awo. Iye wavula mlongo wake ndipo aziyankha mlandu wa cholakwa chakecho.

  • Deuteronomo 27:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “‘Wotembereredwa ndi munthu wogona ndi mlongo wake, mwana wamkazi wa bambo ake kapena mwana wamkazi wa mayi ake.’+ (Anthu onse ayankhe kuti, ‘Zikhale momwemo!’)

  • 2 Samueli 13:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pambuyo pa zinthu zimenezi, zinachitika kuti, Abisalomu+ mwana wa Davide, anali ndi mlongo wake wokongola dzina lake Tamara.+ Ndipo Aminoni+ mwana wa Davide anayamba kukonda kwambiri+ Tamara.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena