2 Samueli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wake wachiwiri anali Kileyabu+ wobadwa kwa Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala, ndipo wachitatu anali Abisalomu+ wobadwa kwa Maaka, mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya ku Gesuri. 1 Mbiri 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 wachitatu Abisalomu,+ wobadwa kwa Maaka+ mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya Gesuri,+ wachinayi Adoniya,+ wobadwa kwa Hagiti,+
3 Mwana wake wachiwiri anali Kileyabu+ wobadwa kwa Abigayeli+ wa ku Karimeli, amene anali mkazi wa Nabala, ndipo wachitatu anali Abisalomu+ wobadwa kwa Maaka, mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya ku Gesuri.
2 wachitatu Abisalomu,+ wobadwa kwa Maaka+ mwana wamkazi wa Talimai+ mfumu ya Gesuri,+ wachinayi Adoniya,+ wobadwa kwa Hagiti,+