1 Mafumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti+ anadzikweza+ n’kumati: “Ineyo ndikhala mfumu yolamulira!”+ Kenako anapangitsa galeta* lake. Analinso ndi amuna okwera pamahatchi,* ndi amuna 50 amene ankathamanga patsogolo pake.+
5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti+ anadzikweza+ n’kumati: “Ineyo ndikhala mfumu yolamulira!”+ Kenako anapangitsa galeta* lake. Analinso ndi amuna okwera pamahatchi,* ndi amuna 50 amene ankathamanga patsogolo pake.+