Miyambo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kunyada kumafikitsa munthu ku chiwonongeko,+ ndipo mtima wodzikuza umachititsa munthu kupunthwa.+ Luka 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti aliyense wodzikweza adzatsitsidwa, ndipo wodzichepetsa adzakwezedwa.”+ Aroma 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+
16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+