Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 11:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kodi kudzikweza kwafika? Ndiye kuti manyazinso afika.+ Koma nzeru zimakhala ndi anthu odzichepetsa.+

  • Miyambo 17:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Aliyense wokonda machimo akukonda kulimbana.+ Aliyense wotalikitsa khomo lake akufunafuna kuwonongedwa.+

  • Miyambo 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu asanagwe, mtima wake umadzikweza,+ ndipo asanapeze ulemerero, amadzichepetsa.+

  • Danieli 4:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+

  • Danieli 5:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 “Koma inuyo a Belisazara,+ amene ndinu mwana wake, simunadzichepetse mumtima mwanu+ ngakhale kuti munali kudziwa zonsezi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena