Luka 12:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pa nthawiyo kapolo amene anadziwa zofuna za mbuye wake koma osakonzekera kubwera kwake, kapena osachita mogwirizana ndi zofuna za mbuye wakeyo, adzakwapulidwa zikoti zambiri.+ Yakobo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero, ngati munthu akudziwa kuchita chabwino koma sakuchichita,+ akuchimwa.+
47 Pa nthawiyo kapolo amene anadziwa zofuna za mbuye wake koma osakonzekera kubwera kwake, kapena osachita mogwirizana ndi zofuna za mbuye wakeyo, adzakwapulidwa zikoti zambiri.+