Yakobo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti pamene pali nsanje+ ndi mtima wokonda mikangano, palinso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+ Yakobo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma nzeru+ yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+
16 Pakuti pamene pali nsanje+ ndi mtima wokonda mikangano, palinso chisokonezo ndi zoipa zamtundu uliwonse.+
17 Koma nzeru+ yochokera kumwamba, choyamba, ndi yoyera,+ kenako yamtendere,+ yololera,+ yokonzeka kumvera, yodzaza ndi chifundo ndi zipatso zabwino,+ yopanda tsankho,+ ndiponso yopanda chinyengo.+