Yoswa 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anali kulamulira kuphiri la Herimoni,+ ku Saleka, ndi ku Basana+ konse, mpaka kukafika kumalire a Agesuri+ ndi Amaakati.+ Anali kulamuliranso hafu ya Giliyadi, mpaka kumalire ndi dera limene Sihoni,+ mfumu ya Hesiboni,+ anali kulamulira.
5 Anali kulamulira kuphiri la Herimoni,+ ku Saleka, ndi ku Basana+ konse, mpaka kukafika kumalire a Agesuri+ ndi Amaakati.+ Anali kulamuliranso hafu ya Giliyadi, mpaka kumalire ndi dera limene Sihoni,+ mfumu ya Hesiboni,+ anali kulamulira.