Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 21:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Anayamba kukhala kumeneko chifukwa Hesiboni unali mzinda wa Sihoni.+ Sihoni inali mfumu ya Aamori,+ ndipo iye ndiye anamenyana ndi mfumu ya Mowabu m’mbuyomo, n’kulanda dziko lonse limene linali m’manja mwake mpaka kuchigwa cha Arinoni.+

  • Deuteronomo 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yonseyo tinaiwononga,+ monga mmene tinachitira ndi Sihoni mfumu ya Hesiboni, mwa kuwononga mzinda uliwonse, amuna, akazi ndi ana aang’ono.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena