Levitiko 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiye chifukwa chake dzikolo n’lodetsedwa, ndipo ndidzalilanga chifukwa cha kulakwa kwake. Pamenepo dzikolo lidzataya anthu ake kunja.+ Deuteronomo 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Tinalandanso mizinda yake yonse pa nthawi imeneyo ndi kuwononga mzinda wina uliwonse.+ Tinapha amuna, akazi ndi ana, ndipo sitinasiye munthu aliyense wamoyo. Ezekieli 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+
25 Ndiye chifukwa chake dzikolo n’lodetsedwa, ndipo ndidzalilanga chifukwa cha kulakwa kwake. Pamenepo dzikolo lidzataya anthu ake kunja.+
34 Tinalandanso mizinda yake yonse pa nthawi imeneyo ndi kuwononga mzinda wina uliwonse.+ Tinapha amuna, akazi ndi ana, ndipo sitinasiye munthu aliyense wamoyo.
6 Mupheretu nkhalamba, anyamata, anamwali, tiana, ndi amayi.+ Koma musayandikire munthu aliyense amene ali ndi chizindikiro,+ ndipo muyambire pamalo anga opatulika.”+ Chotero iwo anayambira kupha akuluakulu amene anali panyumbapo.+