Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 27:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “‘Ngati munthu watenga munthu mnzake, nyama kapena munda wake n’kuupatula kuti ukhale woyera kwa Yehova kwamuyaya,* kapena akapereka munthuyo, nyama kapena munda kwa Mulungu kuti auwononge,+ sungagulitsidwe kapena kuwomboledwa.+ Munthu, nyama kapena munda umenewo ndi wopatulika koposa. Zimenezi ndi za Yehova.

  • Numeri 31:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Tsopano iphani mwana wamwamuna aliyense pakati pa anawa, ndiponso muphe mkazi aliyense amene anagonapo ndi mwamuna.+

  • Deuteronomo 20:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+

  • Deuteronomo 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa muyenera kuwawononga ndithu. Mukawononge Ahiti, Aamori, Akanani, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi,+ monga mmene Yehova Mulungu wanu anakulamulirani.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena