Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+

  • Yeremiya 25:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndipo taonani! pobweretsa tsoka, ndiyamba ndi mzinda wotchedwa ndi dzina langa.+ Kodi inuyo mukufuna kuti musalandire chilango?”’+

      “‘Chilangochi sichikuphonyani pakuti ndikuitana lupanga kuti liukire anthu onse okhala padziko lapansi,’ watero Yehova wa makamu.

  • 1 Petulo 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti ino ndiyo nthawi yoikidwiratu yakuti chiweruzo chiyambe, ndipo chiyambira panyumba ya Mulungu.+ Tsopano ngati chikuyambira pa ife,+ ndiye mapeto a anthu osamvera uthenga wabwino wa Mulungu adzakhala otani?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena