Miyambo 11:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Wolungamatu adzalandira mphoto yake padziko lapansi.+ Ndiye kuli bwanji woipa ndi wochimwa?+ Yeremiya 49:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanena kuti: “Taonani! Ngakhale kuti sanazolowere kumwa za m’kapu, iwo adzamwa ndithu.+ Kodi iwe udzasiyidwa osapatsidwa chilango? Ayi, sudzasiyidwa osapatsidwa chilango pakuti udzamwa ndithu za m’kapumo.”+ Obadiya 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti mmene anthu inu munali kumwera vinyo paphiri langa loyera, ndi mmenenso mitundu ina yonse ya anthu izidzamwera mkwiyo wanga ngati vinyo nthawi zonse.+ Iwo adzamwa ndi kugugudiza mkwiyo wanga, ndipo zidzakhala ngati iwo kunalibe.
12 Yehova wanena kuti: “Taonani! Ngakhale kuti sanazolowere kumwa za m’kapu, iwo adzamwa ndithu.+ Kodi iwe udzasiyidwa osapatsidwa chilango? Ayi, sudzasiyidwa osapatsidwa chilango pakuti udzamwa ndithu za m’kapumo.”+
16 Pakuti mmene anthu inu munali kumwera vinyo paphiri langa loyera, ndi mmenenso mitundu ina yonse ya anthu izidzamwera mkwiyo wanga ngati vinyo nthawi zonse.+ Iwo adzamwa ndi kugugudiza mkwiyo wanga, ndipo zidzakhala ngati iwo kunalibe.