Yeremiya 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinatenga chikho chija chimene chinali m’dzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako.+ Yeremiya 49:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanena kuti: “Taonani! Ngakhale kuti sanazolowere kumwa za m’kapu, iwo adzamwa ndithu.+ Kodi iwe udzasiyidwa osapatsidwa chilango? Ayi, sudzasiyidwa osapatsidwa chilango pakuti udzamwa ndithu za m’kapumo.”+
17 Choncho ndinatenga chikho chija chimene chinali m’dzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako.+
12 Yehova wanena kuti: “Taonani! Ngakhale kuti sanazolowere kumwa za m’kapu, iwo adzamwa ndithu.+ Kodi iwe udzasiyidwa osapatsidwa chilango? Ayi, sudzasiyidwa osapatsidwa chilango pakuti udzamwa ndithu za m’kapumo.”+