1 Mbiri 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Azariya anabereka Seraya,+ ndipo Seraya anabereka Yehozadaki.+ Ezara 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pa zimenezi, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, panali mwamuna wina dzina lake Ezara.+ Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+ Yeremiya 52:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+
7 Pambuyo pa zimenezi, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, panali mwamuna wina dzina lake Ezara.+ Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+
24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+