Yeremiya 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti: Yeremiya 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Iwe watumiza makalata m’dzina lako+ kwa anthu onse amene ali ku Yerusalemu, kwa Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi kwa ansembe onse. Makalatawo ndi onena kuti, Yeremiya 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Zefaniya+ wansembe anawerengera mneneri Yeremiya kalata imeneyi.
21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti:
25 ‘Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti: “Iwe watumiza makalata m’dzina lako+ kwa anthu onse amene ali ku Yerusalemu, kwa Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi kwa ansembe onse. Makalatawo ndi onena kuti,