2 Mafumu 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+ Yeremiya 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti: Yeremiya 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Zefaniya+ wansembe anawerengera mneneri Yeremiya kalata imeneyi. Yeremiya 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mfumu Zedekiya inatumiza Yehukali+ mwana wa Selemiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya+ wansembe kwa mneneri Yeremiya ndi uthenga wakuti: “Chonde, tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu.”+ Yeremiya 52:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+
18 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+
21 Yehova anauza Yeremiya mawu,+ pamene Mfumu Zedekiya+ inatumiza Pasuri+ mwana wa Malikiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya, wansembe, ndi uthenga wakuti:
3 Mfumu Zedekiya inatumiza Yehukali+ mwana wa Selemiya ndi Zefaniya+ mwana wa Maaseya+ wansembe kwa mneneri Yeremiya ndi uthenga wakuti: “Chonde, tipempherere kwa Yehova Mulungu wathu.”+
24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+