Yeremiya 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde tifunsire kwa Yehova+ chifukwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo akufuna kumenyana nafe nkhondo.+ Mwina Yehova adzatichitira imodzi mwa ntchito zake zamphamvu kuti Nebukadirezarayo atichokere.”+ Yeremiya 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kwa mneneri Yeremiya ndi kumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako.+ Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa amene tatsala tilipo ochepa monga mmene ukutioneramu, ngakhale kuti tinalipo anthu ambiri.+
2 “Chonde tifunsire kwa Yehova+ chifukwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo akufuna kumenyana nafe nkhondo.+ Mwina Yehova adzatichitira imodzi mwa ntchito zake zamphamvu kuti Nebukadirezarayo atichokere.”+
2 kwa mneneri Yeremiya ndi kumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako.+ Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa amene tatsala tilipo ochepa monga mmene ukutioneramu, ngakhale kuti tinalipo anthu ambiri.+