Yeremiya 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kwa mneneri Yeremiya nʼkumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako. Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa poyamba tinalipo ambiri koma pano tatsala ochepa+ ngati mmene ukuoneramu.
2 kwa mneneri Yeremiya nʼkumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako. Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa poyamba tinalipo ambiri koma pano tatsala ochepa+ ngati mmene ukuoneramu.