Yeremiya 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 kwa mneneri Yeremiya ndi kumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako.+ Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa amene tatsala tilipo ochepa monga mmene ukutioneramu, ngakhale kuti tinalipo anthu ambiri.+
2 kwa mneneri Yeremiya ndi kumuuza kuti: “Chonde, tikomere mtima ndipo utipempherere kwa Yehova Mulungu wako.+ Pempherera anthu onse amene atsalawa chifukwa amene tatsala tilipo ochepa monga mmene ukutioneramu, ngakhale kuti tinalipo anthu ambiri.+