1 Mbiri 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Azariya anabereka Seraya,+ ndipo Seraya anabereka Yehozadaki.+ Ezara 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pambuyo pa zimenezi, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, panali mwamuna wina dzina lake Ezara.+ Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+
7 Pambuyo pa zimenezi, mu ulamuliro wa mfumu Aritasasita+ ya ku Perisiya, panali mwamuna wina dzina lake Ezara.+ Iye anali mwana wa Seraya.+ Seraya anali mwana wa Azariya, Azariya anali mwana wa Hilikiya,+