2 Mafumu 22:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe,+ ukamuuze kuti asonkhanitse pamodzi ndalama zonse+ zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo+ atolera kwa anthu. 1 Mbiri 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa magulu a alonda a pazipatawa, ntchito ya atsogoleri awo inali yofanana ndi ya abale awo,+ ndipo inali yotumikira panyumba ya Yehova.
4 “Pita kwa Hilikiya+ mkulu wa ansembe,+ ukamuuze kuti asonkhanitse pamodzi ndalama zonse+ zimene zikubwera kunyumba ya Yehova,+ zimene alonda a pakhomo+ atolera kwa anthu.
12 Pa magulu a alonda a pazipatawa, ntchito ya atsogoleri awo inali yofanana ndi ya abale awo,+ ndipo inali yotumikira panyumba ya Yehova.