2 Mbiri 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mfumuyo inawauza zochita ndipo anapanga bokosi+ n’kuliika panja, pachipata cha nyumba ya Yehova.
8 Tsopano mfumuyo inawauza zochita ndipo anapanga bokosi+ n’kuliika panja, pachipata cha nyumba ya Yehova.