1 Mbiri 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anachita maere+ powagawira ntchito yoti azichita. Pochita maerewo, onse anali chimodzimodzi. Sanali kuyang’ana kuti uyu ndi wamng’ono kapena wamkulu,+ katswiri+ kapena wophunzira kumene.
8 Kenako anachita maere+ powagawira ntchito yoti azichita. Pochita maerewo, onse anali chimodzimodzi. Sanali kuyang’ana kuti uyu ndi wamng’ono kapena wamkulu,+ katswiri+ kapena wophunzira kumene.