Miyambo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+ Miyambo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Maere amathetsa mikangano,+ ndipo amalekanitsa ngakhale anthu amphamvu.+ Machitidwe 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja.
26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja.