Numeri 26:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Njira yokha imene ugawire dzikolo ndiyo mwa kuchita maere basi.+ Onse alandire cholowacho potsata mayina a mafuko a makolo awo. Yoswa 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo Yoswa anawachitira maere pamaso pa Yehova+ ku Silo. Kumeneko Yoswa anagawa dzikolo n’kupereka gawo limodzilimodzi ku mafuko a ana a Isiraeli.+ Miyambo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Maere amathetsa mikangano,+ ndipo amalekanitsa ngakhale anthu amphamvu.+ Machitidwe 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja.
55 Njira yokha imene ugawire dzikolo ndiyo mwa kuchita maere basi.+ Onse alandire cholowacho potsata mayina a mafuko a makolo awo.
10 ndipo Yoswa anawachitira maere pamaso pa Yehova+ ku Silo. Kumeneko Yoswa anagawa dzikolo n’kupereka gawo limodzilimodzi ku mafuko a ana a Isiraeli.+
26 Atatero anachita maere+ pa iwo, ndipo maerewo anagwera Matiya. Choncho iye anamuphatikiza pa atumwi 11+ aja.