Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 34:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chotero Mose anauza ana a Isiraeli kuti: “Ili ndilo dziko limene ligawidwe kwa inu mwa maere+ monga cholowa chanu. Lidzagawidwa kwa inu monga momwe Yehova analamulira kuti lipatsidwe kwa mafuko 9 ndi hafu.+

  • Yoswa 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anagawira cholowacho mafuko 9 ndi hafu, mwa kuchita maere,+ monga mmene Yehova analamulira kudzera mwa Mose.+

  • Yoswa 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo anakaonekera pamaso pa wansembe Eleazara,+ Yoswa mwana wa Nuni, ndi atsogoleri, ndi kuwauza kuti: “Yehova ndiye analamula Mose kuti atipatse cholowa pakati pa abale athu.”+ Choncho anawapatsa cholowa pakati pa abale a bambo awo, pomvera lamulo la Yehova.+

  • Yoswa 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma anthu inu, mukagawe dzikolo m’zigawo 7 ndipo mukazilembe. Mukakatero, mukabwere nazo kuno kwa ine kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.

  • Miyambo 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena