Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 26:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Njira yokha imene ugawire dzikolo ndiyo mwa kuchita maere basi.+ Onse alandire cholowacho potsata mayina a mafuko a makolo awo.

  • Numeri 33:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Mukagawire dzikolo kwa mabanja anu monga cholowa chanu mwa kuchita maere.+ Banja la anthu ambiri mukaliwonjezere cholowa chawo, ndipo banja la anthu ochepa mukalichepetsere cholowa chawo.+ Malo alionse amene maere akagwere banja, akapatsidwe kwa banjalo.+ Mukagawane malowo potsata mafuko a makolo anu.+

  • Yoswa 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anagawira cholowacho mafuko 9 ndi hafu, mwa kuchita maere,+ monga mmene Yehova analamulira kudzera mwa Mose.+

  • Miyambo 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+

  • Machitidwe 13:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndipo atawononga mitundu 7 m’dziko la Kanani, anagawa dzikolo kwa Aisiraeli mwa kuchita maere.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena