Yoswa 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malire a gawo+ la ana a Yosefe+ anayambira kumtsinje wa Yorodano+ kufupi ndi Yeriko kukafika kumadzi a Yeriko chakum’mawa, mpaka kuchipululu chochokera ku Yeriko kukafika kudera lamapiri la Beteli.+ Yoswa 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Maere+ oyamba anagwera fuko la ana a Benjamini+ potsata mabanja awo, ndipo gawo limene anapatsidwa linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+
16 Malire a gawo+ la ana a Yosefe+ anayambira kumtsinje wa Yorodano+ kufupi ndi Yeriko kukafika kumadzi a Yeriko chakum’mawa, mpaka kuchipululu chochokera ku Yeriko kukafika kudera lamapiri la Beteli.+
11 Maere+ oyamba anagwera fuko la ana a Benjamini+ potsata mabanja awo, ndipo gawo limene anapatsidwa linali pakati pa ana a Yuda+ ndi ana a Yosefe.+