Miyambo 16:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+ Numeri 26:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 “Anthu amenewa uwagawire dzikoli malinga ndi chiwerengero cha mayinawo, kuti likhale cholowa chawo.+
53 “Anthu amenewa uwagawire dzikoli malinga ndi chiwerengero cha mayinawo, kuti likhale cholowa chawo.+