Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Anagawira cholowacho mafuko 9 ndi hafu, mwa kuchita maere,+ monga mmene Yehova analamulira kudzera mwa Mose.+

  • 1 Samueli 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini malinga ndi mabanja awo, ndipo banja la Amatiri linasankhidwa.+ Pamapeto pake, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Choncho anayamba kum’funafuna, koma sanam’peze.

  • Nehemiya 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano akalonga+ a anthuwo anali kukhala m’Yerusalemu.+ Anthu ena onse anachita maere+ kuti apeze munthu mmodzi mwa anthu 10 alionse woti akakhale m’Yerusalemu, mzinda woyera,+ ndiponso kuti anthu ena 9 otsalawo akhale m’mizinda ina.

  • Miyambo 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Maere amaponyedwa pamwendo,+ koma zonse zimene maerewo amasonyeza zimachokera kwa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena