Yoswa 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Potsirizira pake anauza a m’nyumba ya Zabidi kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha. Ndipo Akani mwana wa Karami, mwana wa Zabidi, mwana wa Zera, wa fuko la Yuda, anasankhidwa.+ Machitidwe 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma kuchokera pamenepo anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Chotero Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.
18 Potsirizira pake anauza a m’nyumba ya Zabidi kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha. Ndipo Akani mwana wa Karami, mwana wa Zabidi, mwana wa Zera, wa fuko la Yuda, anasankhidwa.+
21 Koma kuchokera pamenepo anthuwo ananena kuti akufuna mfumu.+ Chotero Mulungu anawapatsa Sauli mwana wa Kisi, munthu wa fuko la Benjamini,+ ndipo anakhala mfumu yawo kwa zaka 40.