Yoswa 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anauza mabanja a m’fuko la Yuda kufika pamaso pa Mulungu, ndipo banja la Zera linasankhidwa. Kenako anauza banja la Zera+ kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha, ndipo Zabidi anasankhidwa.
17 Kenako anauza mabanja a m’fuko la Yuda kufika pamaso pa Mulungu, ndipo banja la Zera linasankhidwa. Kenako anauza banja la Zera+ kufika pamaso pa Mulungu, mwamuna aliyense wamphamvu payekhapayekha, ndipo Zabidi anasankhidwa.