-
2 Mafumu 12:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Tsopano Yehoasi anauza ansembe kuti:+ “Ndalama zonse zimene anthu akubweretsa kunyumba ya Yehova+ za zopereka zopatulika,+ kutanthauza ndalama za msonkho zimene munthu aliyense akupereka,+ ndalama zoperekedwa ndi anthu amene achita chowinda,+ ndiponso ndalama zonse zimene munthu aliyense watsimikiza mumtima mwake kuti abweretse kunyumba ya Yehova,+
-