1 Mbiri 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira+ Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide amene inalanda ku mitundu yonse,+ kuchokera ku Edomu, ku Mowabu,+ kwa ana a Amoni,+ Afilisiti,+ ndi Aamaleki.+ 2 Mbiri 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthuwo anapitiriza kubweretsa zopereka,+ chakhumi,+ ndi zinthu zopatulika. Iwo ankabweretsa zimenezi mokhulupirika.+ Konaniya Mlevi ndiye anali kuyang’anira monga mtsogoleri, ndipo Simeyi m’bale wake anali wachiwiri wake.
11 Zinthu zimenezi Mfumu Davide inazipatulira+ Yehova pamodzi ndi siliva ndi golide amene inalanda ku mitundu yonse,+ kuchokera ku Edomu, ku Mowabu,+ kwa ana a Amoni,+ Afilisiti,+ ndi Aamaleki.+
12 Anthuwo anapitiriza kubweretsa zopereka,+ chakhumi,+ ndi zinthu zopatulika. Iwo ankabweretsa zimenezi mokhulupirika.+ Konaniya Mlevi ndiye anali kuyang’anira monga mtsogoleri, ndipo Simeyi m’bale wake anali wachiwiri wake.