1 Samueli 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Davide pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kukathira nkhondo Agesuri,+ Agirezi ndi Aamaleki.+ Mitundu imeneyi inali kukhala m’dera loyambira ku Telami+ kukafika ku Shura,+ mpaka kukafika kudziko la Iguputo. 1 Samueli 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho Davide anatenga nkhosa zonse ndi ng’ombe zonse za Aamaleki komanso ziweto zonse zimene Aamaleki anawalanda. Kenako iwo anati: “Izi ndi zofunkha za Davide.”+
8 Ndiyeno Davide pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kukathira nkhondo Agesuri,+ Agirezi ndi Aamaleki.+ Mitundu imeneyi inali kukhala m’dera loyambira ku Telami+ kukafika ku Shura,+ mpaka kukafika kudziko la Iguputo.
20 Choncho Davide anatenga nkhosa zonse ndi ng’ombe zonse za Aamaleki komanso ziweto zonse zimene Aamaleki anawalanda. Kenako iwo anati: “Izi ndi zofunkha za Davide.”+