1 Samueli 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Davide ndi amuna amene ankayenda naye ankapita kukamenyana ndi Agesuri,+ Agirezi ndi Aamaleki.+ Anthu amenewa ankakhala mʼdera loyambira ku Telami kukafika ku Shura,+ mpaka kudziko la Iguputo.
8 Davide ndi amuna amene ankayenda naye ankapita kukamenyana ndi Agesuri,+ Agirezi ndi Aamaleki.+ Anthu amenewa ankakhala mʼdera loyambira ku Telami kukafika ku Shura,+ mpaka kudziko la Iguputo.