Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:17, 18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Isimaeli anakhala ndi moyo zaka 137. Kenako anamwalira ndipo anaikidwa mʼmanda ngati mmene anachitira ndi makolo ake. 18 Mbadwa zake zinayamba kukhala ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyandikana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Iwo anakhala pafupi ndi abale awo onse.*+

  • Ekisodo 15:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kenako Mose anatsogolera Isiraeli kuchoka ku Nyanja Yofiira ndipo analowa mʼchipululu cha Shura. Iwo anayenda mʼchipululumo kwa masiku atatu, koma sanapeze madzi.

  • 1 Samueli 15:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako Sauli anapha Aamaleki+ kuyambira ku Havila+ mpaka ku Shura,+ pafupi ndi Iguputo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena