1 Samueli 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Davide pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kukathira nkhondo Agesuri,+ Agirezi ndi Aamaleki.+ Mitundu imeneyi inali kukhala m’dera loyambira ku Telami+ kukafika ku Shura,+ mpaka kukafika kudziko la Iguputo.
8 Ndiyeno Davide pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye anapita kukathira nkhondo Agesuri,+ Agirezi ndi Aamaleki.+ Mitundu imeneyi inali kukhala m’dera loyambira ku Telami+ kukafika ku Shura,+ mpaka kukafika kudziko la Iguputo.