Genesis 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anakhala m’mahema kuyambira ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyang’anana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Anakhala pafupi ndi abale awo onse.+ Ekisodo 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Mose anauza Isiraeli kuti anyamuke pa Nyanja Yofiira ndipo analowa m’chipululu cha Shura.+ Iwo anayenda m’chipululumo kwa masiku atatu, koma sanapeze madzi.+
18 Iwo anakhala m’mahema kuyambira ku Havila+ pafupi ndi Shura+ moyang’anana ndi Iguputo, mpaka ku Asuri. Anakhala pafupi ndi abale awo onse.+
22 Kenako Mose anauza Isiraeli kuti anyamuke pa Nyanja Yofiira ndipo analowa m’chipululu cha Shura.+ Iwo anayenda m’chipululumo kwa masiku atatu, koma sanapeze madzi.+