Genesis 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwanayo adzakhala ngati mbidzi. Dzanja lake lidzalimbana ndi aliyense, ndipo dzanja la aliyense lidzalimbana naye.+ Iye adzamanga msasa pamaso pa abale ake onse.”+
12 Mwanayo adzakhala ngati mbidzi. Dzanja lake lidzalimbana ndi aliyense, ndipo dzanja la aliyense lidzalimbana naye.+ Iye adzamanga msasa pamaso pa abale ake onse.”+